EXCELL KHAMA ft DECORIJO – CHAMBA si EMBASSY full lylics

Artist: Excell Khama ft. Decorijoh | Title: Chamba Si Embassy | Album: Single

INTRO
Uuuu Hahaaa Boosting Levo Yeh! / Excell khama!!

HOOK
Osamafananiza zinthu ziwiri / nfana osatha ndi wa skill / a lie and something that is real / kuyambila lero choti mudziwe / CHAMBA x4 / si EMBASSY x3 / chamba !

VERSE 1 – (EXCELL KHAMA)
Osamapanga compare / nfana wa skill ndi okopera / pa zabho manja kuombera / osati ndi nfuti kufuna kuombera / Secret of life u wana know / if you earn less don’t spend more / in your doings don’t expect more / to avoid noise respect more / nde pliz don’t / osafananiza miyala m’dothi / ndine oyaka moto koloboi / sindimagwera ngati goloboi / ndiziulure dzina ndine doloboi / ase mwezi si week / Barley si weed / tsitsi si wig / they differ they can’t match-in / singano adha si machine / masese si Malawi gin /always do what you imagine /enawa si ma friends ndinawatulukira pakhomo-pakhomo / Nyimbo ndimazitengera pamgon’go-pamgon’go / zanga zuyenda pang’ono-pang’ono / ngati mwina ndi nkhono ndi nkhono

HOOK
Osamafananiza zinthu ziwiri / nfana osatha ndi wa skill / a lie and something that is real / kuyambila lero choti mudziwe / CHAMBA x4 / si EMBASSY x3 / chamba !

VERSE 2 – (DECORIJO)
CHAMBA si EMBASSY / verse si chorus / Deco si mbola ase / koma kuluma ngati mavu nkhomola ase / osamanama mukakhala kuti mwationa pa kanema / sitisewera ndi ana or atakhala kuti akusewera ngati Neymar / si mphavu , si nkhondo , zoimba mwaphuma ayi / CG BEATS nd Cafe lyric yanga nd braai / Mafana amu Lilongwe koma kukhala mu Dubai / ndine ofana ovaya ngat link ndinanena kale bye-bye / CHAMBA si EMBASSY / mpeni Si Nyemba ase / ndanva kuti zikamandiyendera bwino ukumakwiya ase / koma pepa ase / chonde usinthe ase / sungamapange zamunthu nkumapanga ndalama ase