Get to know Rude P

Rude P – Born Peter Nazimela

Rude P ndi mwana wa chitatu wa Bambo ndi Mai Nazimera Dzina lake lenileni ndi Peter Nazimela. Rude P anayamba kuimba m’chaka cha 2007 chifukwa chosangalatsidwa ndi nyimbo za Annie Matumbi patapita ka nthawi adasintha kuyamba kukonda oyimba ena monga Jolly Bro (JB) komaso Young D omwe a maimba chamba cha Hip Hop.

I released my first single on 2012 on my graduation ceremony under SATA crew and my fellow students acknowledged me though my mom doesn’t like me to be a musician for I use to beat tables and flow freestyles in the house with my young brother.

Mbiri ya Rude P

Pofika pano ali ndi nyimbo 14 like Malita, Show me, Lets get married, I don’t care and many more. He also has worked with some artists like Yo Maps, G1, Smart Deltar from Zambia, Tay Tol from South Africa and Major Gwanzy.

Ndi malimbikira kuti ndi tulutse nyimbo zogwira mtima komaso ndinalonjeza mai anga kuti sidzaimba nyimbo yonyoza kapena yokhala ndi mau olakwika.

Rude P ku lankhulana ndi D West (Interviewer)

He currently is just releasing singles. He does not have any album or Extended Play ( EP) he only told us that he has big plans with Major Gwazy so we should expect something to be released one day though he didn’t disclose any of their plans.


Pongotchulapo za mavuto omwe wakumana nawo wafotokoza kuti vuto lalikulu ndi la za chuma chifukwa masiku ano ma studio abwino ndi odula komaso pena amalipira ndalama zambiri kwa anthu amene waimba nawo nyimbo.
Pamapeto pake Rude P analimbikisa oimba a chichepere kuti adzilimbikira pa chomwe akufuna ku dzakhala komaso adziunikira bwino nyimbo zawo asanapite nazo ku studio.

Iyi inali mbiri ya Rude P next week tibweletsa nso oimba wina wa chisodzera.