Meet Jolasto

Last Monday on 18 January 2021 on Team Ndekha Muzik tinali ndi interview with JOLASTO
Hosted by D West

Jolasto amachokela ku Chilimba mu mzinda wa Blantyre ndipo anayamba zoimbazi m’chaka cha 2015 pamene akakhala pafupi ndi ma producer onjambula nyimbo.

Pofika pano ali ndi nyimbo pafupifupi 30 koma alibe EP kapena Album. Zina mwa nyimbo zake ndi ngati Tisakhe Ndani feat Lucius Banda [Download Here], Abwenzi a padziko, Iwe Sir (Adidas cover by Martse), Dekha and Mutenge Matenda. Wa imbaponso ndi oimba odziwika ngati Walycris.

My favourite artists in Malawi are Martse and Macelba. In this year 2021 am going to release yet more songs

Anatero Jolasto

Pa khani ya Lucius Banda anati there is no relationship iye nyimboyo inangomusangalatsa that’s why anaimbaso ndipo anali atapepha chilorezo and za Adidas cover he said for the love he has with Martse Music anaimba cover ija koma pa nalibe beef ina iliyonse.

Pomaliza Jolasto anapepha anthu omutsata kuti asasiye kumukonda komaso anati mukhoza kumpeza pa Facebook Jolasto Afulika pa instgram ndi Afulika.